Mlaliki 8:10 BL92

10 Ndipo ndinaona oipa alikuikidwa m'manda ndi kupita; ndipo omwe anacita zolungama anacokera ku malo opatulika a ku mudzi nawaiwala; icinso ndi cabe.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 8

Onani Mlaliki 8:10 nkhani