Yeremiya 37:14 BL92

14 Ndipo anati Yeremiya, Kunama kumeneko; ine sindipandukira kwa Akasidi; koma sanamvera iye; ndipo Iriya anamgwira Yeremiya, nanka naye kwa akuru.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 37

Onani Yeremiya 37:14 nkhani