Yeremiya 50:28 BL92

28 Mau a iwo akuthawa akupulumuka m'dziko la Babulo, kuti alalikire m'Ziyoni kubwezera cilango kwa Yehova Mulungu wathu, kubwezera cilango cifukwa ca Kacisi wace.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:28 nkhani