Yesaya 13:18 BL92

18 Mauta ao adzatha anyamata; ndipo sadzacitira cisoni cipatso ca mimba; diso lao silidzaleka ana.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 13

Onani Yesaya 13:18 nkhani