Yoswa 7:22 BL92

22 Pamenepo Yoswa anatuma mithenga, iwo nathamangira kuhema; ndipo taonani, zidabisika m'hema mwace ndi siliva pansi pace.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 7

Onani Yoswa 7:22 nkhani