1 Ndipo kunacitika caka cacinai ca mfumu Dariyo, mau a Yehova anadza kwa Zekariya tsiku lacinai la mwezi wacisanu ndi cinai, ndiwo Kisilevi.
Werengani mutu wathunthu Zekariya 7
Onani Zekariya 7:1 nkhani