Zekariya 8:4 BL92

4 Atero Yehova wa makamu: M'miseu ya Yerusalemu mudzakhalanso amuna ndi akazi okalamba, yense ndi ndodo yace m'dzanja lace cifukwa ca ukalamba wace.

Werengani mutu wathunthu Zekariya 8

Onani Zekariya 8:4 nkhani