8 Koma ngakhale ife, kapena mngelo wocokera Kumwamba, ngati akakulalikireni uthenga wabwino wosati umene tidakulalikirani ife, akhale wotembereredwa.
Werengani mutu wathunthu Agalatiya 1
Onani Agalatiya 1:8 nkhani