Mateyu 26:26 BL92

26 Ndipo pamene iwo analinkudya, Yesu anatenga mkate, nadalitsa, naunyema; ndipo m'mene anapatsa kwa ophunzira, anati, Tengani, idyani; ici ndi thupi langa.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 26

Onani Mateyu 26:26 nkhani