Filemoni 1:14 BL92

14 koma wopanda kudziwa mtima wako sindinafuna kucita kanthu; kuti ubwino wako usakhale monga mokakamiza, komatu mwaufulu.

Werengani mutu wathunthu Filemoni 1

Onani Filemoni 1:14 nkhani