8 Kwerani ku dziko la mapiri, ndi kukwera nayo mitengo, nimumange nyumbayi; ndipo kudzandikomera, ndipo ndidzalemekezedwa, ati Yehova.
Werengani mutu wathunthu Hagai 1
Onani Hagai 1:8 nkhani