Hagai 2:3 BL92

3 Adatsala ndani mwa inu amene anaona nyumba iyi m'ulemerero wace woyamba? ndipo muiona yotani tsopano? Kodi siikhala m'maso mwanu ngati cabe?

Werengani mutu wathunthu Hagai 2

Onani Hagai 2:3 nkhani