16 Pakuti monga munamwa pa phiri langa lopatulika, momwemo amitundu onse adzamwa kosalekeza; inde adzamwa, nadzameza, nadzakhala monga ngati sanalipo.
Werengani mutu wathunthu Obadiya 1
Onani Obadiya 1:16 nkhani