Obadiya 1:3 BL92

3 Kudzikuza kwa mtima wako kwakunyenga, iwe wokhala m'mapanga a thanthwe, iwe pokhala pako pamwamba, wakunena m'mtima mwace, Adzanditsitsira pansi ndani?

Werengani mutu wathunthu Obadiya 1

Onani Obadiya 1:3 nkhani