Yuda 1:23 BL92

23 koma ena 6 muwapulumutse ndi kuwakwatula kumoto; koma ena muwacitire cifundo ndi mantha, 7 nimudane naonso maraya ocitidwa mawanga ndi thupi

Werengani mutu wathunthu Yuda 1

Onani Yuda 1:23 nkhani