Habakuku 1:15 BL92

15 Aziwedza zonse ndi mbedza, azigwira m'ukonde wace, nazisonkhanitsa m'khoka mwace; cifukwa cace asekera nakondwerera.

Werengani mutu wathunthu Habakuku 1

Onani Habakuku 1:15 nkhani