2 Yehova, ndinamva mbiri yanu ndi mantha;Yehova, tsitsimutsani nchito yanu pakati pa zaka,Pakati pa zaka mudziwitse;Pa mkwiyo mukumbukile cifundo.
Werengani mutu wathunthu Habakuku 3
Onani Habakuku 3:2 nkhani