Habakuku 3:8 BL92

8 Kodi Yehova anaipidwa nayo mitsinje?Mkwiyo wanu unali pamitsinje kodi,Kapena ukali wanu panyanja,Kuti munayenda pa akavalo anu,Pa magareta anu a cipulumutso?

Werengani mutu wathunthu Habakuku 3

Onani Habakuku 3:8 nkhani