5 Mapiri agwedezeka cifukwa ca Iye, ndi zitunda zisungunuka; ndi dziko lapansi likwezeka pamaso pace, ndi maiko ndi onse okhala m'mwemo.
Werengani mutu wathunthu Nahumu 1
Onani Nahumu 1:5 nkhani