Nahumu 2:10 BL92

10 Ndiye mopanda kanthu mwacemo ndi mwacabe, ndi wopasuka; ndi mtima usungunuka, ndi maondo aombana, ndi m'zuuno zonse muwawa, ndi nkhope zao zatumbuluka.

Werengani mutu wathunthu Nahumu 2

Onani Nahumu 2:10 nkhani