Nahumu 2:2 BL92

2 Pakuti Yehova abwezeranso ukulu wace wa Yakobo ngati ukulu wace wa Israyeli; pakuti okhuthula anawakhuthula, naipsa nthambi zace za mpesa.

Werengani mutu wathunthu Nahumu 2

Onani Nahumu 2:2 nkhani