10 Koma iye anatengedwa, analowa ndende; ana ace a makanda anaphwanyika polekeza pace pa miseu yace yonse; ndi pa omveka ace anacita maere, ndi akulu ace onse anamangidwa maunyolo.
Werengani mutu wathunthu Nahumu 3
Onani Nahumu 3:10 nkhani