13 Taona, anthuako m'kati mwako akunga akazi; zipata za dziko lako zatsegulidwira adani ako papakuru; moto watha mipingiridzo yako.
Werengani mutu wathunthu Nahumu 3
Onani Nahumu 3:13 nkhani