Nahumu 3:7 BL92

7 Ndipo kudzali kuti onse akupenyerera iwe adzakuthawa, nadzati, Nineve wapasuka, adzamlira maliro ndani? ndidzakufunira kuti akukutonthoza?

Werengani mutu wathunthu Nahumu 3

Onani Nahumu 3:7 nkhani