Yona 1:10 BL92

10 Pamenepo amunawo anaopa kwambiri, nati kwa iye, Ici nciani wacicita? Pakuti amunawo anadziwa kuti anathawa pamaso pa Yehova, popeza adawauza.

Werengani mutu wathunthu Yona 1

Onani Yona 1:10 nkhani