6 Ndinatsikira ku matsinde a mapiri,Mipingiridzo ya dziko inanditsekereza kosatha;Koma munandikwezera moyo wanga kuucotsa kucionongeko, Yehova Mulungu wanga.
Werengani mutu wathunthu Yona 2
Onani Yona 2:6 nkhani