Zefaniya 3:17 BL92

17 Yehova Mulungu wako ali pakati pako, wamphamvu wakupulumutsa; adzakondwera nawe ndi cimwemwe, adzakhala wopanda thamo m'cikondi cace; adzasekerera nawe ndi kuyimbirapo.

Werengani mutu wathunthu Zefaniya 3

Onani Zefaniya 3:17 nkhani