Zefaniya 3:7 BL92

7 Ndinati, Zedi udzandiopa Ine, udzalola kulangizidwa, kuti pokhala pace pasaonongeke, monga mwa zonse ndamuikira; koma analawirira mamawa, nabvunditsa macitidwe ao onse.

Werengani mutu wathunthu Zefaniya 3

Onani Zefaniya 3:7 nkhani