Akolose 1:20 BL92

20 mwa Iyenso kuyanjanitsa zinthu zonse kwa iye mwini, atacita mtendere mwa mwazi wa mtanda wace; mwa Iyetu, kapena za padziko, kapena za m'mwamba.

Werengani mutu wathunthu Akolose 1

Onani Akolose 1:20 nkhani