6 umene udafikira kwa inu; monganso m'dziko lonse lapansi umabala zipatso, numakula, monganso mwa inu; kuyambira tsikulo mudamva nimunazindildra cisomo ca Mulungu m'coonadi;
Werengani mutu wathunthu Akolose 1
Onani Akolose 1:6 nkhani