1 Pakuti ndifuna kuti inu mudziwe nkhawa imene ndiri nayo cifukwa ca inu, ndi iwowa a m'Laodikaya, ndi onse amene sanaone nkhope yanga m'thupi;
Werengani mutu wathunthu Akolose 2
Onani Akolose 2:1 nkhani