13 kulolerana wina ndi mnzace, ndi kukhululukirana eni okha, ngati wina ali naco cifukwa pa mnzace; monganso Ambuye anakhululukira inu, teroni inunso;
Werengani mutu wathunthu Akolose 3
Onani Akolose 3:13 nkhani