8 Koma tsopano tayani inunso zonsezi: mkwiyo, kupsa mtima, dumbo, mwano, zonyansa zoturuka m'kamwa mwanu:
Werengani mutu wathunthu Akolose 3
Onani Akolose 3:8 nkhani