Tito 1:11 BL92

11 amene ayenera kutsekedwa pakamwa; ndiwo amene apasula mabanja banja lonse, ndi kuphunzitsa zosayenera cifukwa ca cisiriro conyansa.

Werengani mutu wathunthu Tito 1

Onani Tito 1:11 nkhani