4 kwa Tito, mwana wanga weni weni monga mwa cikhulupiriro ca ife tonse: Cisomo ndi mtendere za kwa Mulungu Atate ndi Kristu Yesu Mpulumutsi wathu.
Werengani mutu wathunthu Tito 1
Onani Tito 1:4 nkhani