Tito 2:12 BL92

12 ndi kutiphunzitsa ife kuti, pokana cisapembedzo ndi zilakolako za dziko lapansi, tikhale ndi moyo m'dziko lino odziletsa, ndi olungama, ndi opembedza;

Werengani mutu wathunthu Tito 2

Onani Tito 2:12 nkhani