Tito 2:3 BL92

3 Momwemonso akazi okalamba akhale nao makhalidwe oyenera anthu oyera, osadierekeza, osakodwa naco cikondi ca pavinyo, akuphunzitsa zokoma;

Werengani mutu wathunthu Tito 2

Onani Tito 2:3 nkhani