Tito 3:12 BL92

12 Pamene ndikatuma Artema kwa iwe, kapena Tukiko, cita cangu kudza kwa ine ku Nikopoli: pakuti ndatsimikiza mtima kugonerako nyengo yacisanu.

Werengani mutu wathunthu Tito 3

Onani Tito 3:12 nkhani