Mika 7:14 BL92

14 Mudyetse anthu anu ndi ndodo yanu, nkhosa za colowa canu zokhala pa zokha m'nkhalango pakati pa Karimeli, zidye m'Basana ndi m'Gileadi masiku a kale lomwe.

Werengani mutu wathunthu Mika 7

Onani Mika 7:14 nkhani