14 Nakweza iwo mau ao, naliranso misozi; ndi Olipa anampsompsona mpongozi wace, koma Rute anamkangamira.
Werengani mutu wathunthu Rute 1
Onani Rute 1:14 nkhani