17 Ndi akazi anansi ace anamucha dzina, ndi kuti, Kwa Naomi kwambadwira mwana; namucha dzina lace Ohedi; ndiye atate wa Jese atate wa Davide.
Werengani mutu wathunthu Rute 4
Onani Rute 4:17 nkhani