Yona 1:12 BL92

12 Ndipo anati nao, Mundinyamule ndi kundiponya m'nyanja, momwemo nyanja idzacitira inu bata; pakuti ndidziwa kuti namondwe wamkuru amene wakugwerani cifukwa ca ine.

Werengani mutu wathunthu Yona 1

Onani Yona 1:12 nkhani