Yona 1:13 BL92

13 Koma amunawo anapalasa kubwerera kumtunda, koma sanathe; pakuti namondwe wa panyanja anakulakula mokomana nao.

Werengani mutu wathunthu Yona 1

Onani Yona 1:13 nkhani