Yona 1:6 BL92

6 Ndipo mwini combo anadza kwa iye, nanena naye, Utani iwe wam'tulo? uka, itana Mulungu wako, kapena Mulunguyo adzatikumbukila tingatayike.

Werengani mutu wathunthu Yona 1

Onani Yona 1:6 nkhani