Yona 3:5 BL92

5 Ndipo anthu a Nineve anakhulupirira Mulungu, nalalikira cosala, nabvala ciguduli, kuyambira wamkuru kufikira wamng'ono wa iwowa.

Werengani mutu wathunthu Yona 3

Onani Yona 3:5 nkhani