17 Mbeu zaola pansi pa zibuluma zao; zosungiramo zaonongeka, nkhokwe zapasuka; pakuti tirigu wakwinyata.
Werengani mutu wathunthu Yoweli 1
Onani Yoweli 1:17 nkhani