Yoweli 1:19 BL92

19 Ndipfuulira kwa Inu Yehova, pakuti moto wapsereza mabusa a m'cipululu, ndi malawi a moto anatentha mitengo yonse ya kuthengo,

Werengani mutu wathunthu Yoweli 1

Onani Yoweli 1:19 nkhani