Yoweli 2:16 BL92

16 sonkhanitsani anthu, patulani msonkhano, memezani akulu akulu, sonkhanitsani ana ndi oyamwa mawere; mkwati aturuke m'cipinda mwace, ndi mkwatibwi m'mogona mwace.

Werengani mutu wathunthu Yoweli 2

Onani Yoweli 2:16 nkhani