26 Ndipo mudzadyaidya ndi kukhuta, nimudzalemekeza dzina la Yehova Mulungu wanu, amene anacita nanu modabwiza; ndi anthu anga sadzacita manyazi nthawi zonse.
Werengani mutu wathunthu Yoweli 2
Onani Yoweli 2:26 nkhani