Yoweli 3:19 BL92

19 Aigupto adzasanduka bwinja, ndi Edomu adzasanduka cipululu copanda kanthu, cifukwa ca ciwawaci anawacitira ana a Yuda; popeza anakhetsa mwazi wosacimwa m'dziko lao.

Werengani mutu wathunthu Yoweli 3

Onani Yoweli 3:19 nkhani